Songtexte.com Drucklogo

Yampeza Songtext
von Eli Njuchi

Yampeza Songtext

Njuchi
Sting
Ndinampeza
Wondikonda opanda malire
Ay yeah yeah

Moni wakwana, a perfectionist Bandawe, (Bandawe)
You wish you had me nawe, eya sungakane
You had your time and I told you kulibeso wina ineyo
Munali mukana searcher, a perfectionist Bandawe

Ntchito yophweka bambo
Ndimkati mundikonde bambo
Mungondipatsa nthawi bambo
You had your time and I told you kulibeso wina ineyo
Ntchito yophweka bambo
Ndimkati mundikonde bambo
Mungondipatsa nthawi bambo
He had his time and I told him, zibwanazi abetsa dona


Pano mbiri yampeza
Save the date yampeza
Panopa news yampeza
Invite yampeza
Mbiri yampeza
Save the date yampeza
Panopa news yampeza
Akuti fever yampeza

Yampeza, mbiri
Save the date, yampeza
Invite yampeza
Yampeza, mbiri
Save the date, yampeza
Akuti fever yampeza

Sungavomeleze
When I meet your fam amangoti ndinebe mula wawo
Mpaka lero sadziwa zomwe anandipanga mwana wawo
Shame on you, shame on you yeah
Komwe uliko, komwe aliko
Akumwa ma painkiller
Life yabowa akumangolira
Amandi caller ati adzimangilira, (ey yeah)
Sizikusintha zaponda mwala
Akumwa ma painkiller
Life yabowa akumangolira
Amandi caller ati adzimangilira, (koma)
Sizikusintha zaponda mwala


Pano mbiri yampeza
Save the date yampeza
Panopa news yampeza
Invite yampeza
Mbiri yampeza
Save the date yampeza
Panopa news yampeza
Akuti fever yampeza

Yampeza, mbiri
Save the date, yampeza
Invite yampeza
Yampeza, mbiri
Save the date, yampeza
Akuti fever yampeza

Mbiri yampeza
Save the date yampeza
Panopa news yampeza
Invite yampeza
Mbiri yampeza
Save the date yampeza
Panopa news yampeza
Akuti fever yampeza ah

Yeah
Shame on you, shame on you yeah
Because you never knew
You never knew, you never knew
Oh no
Sispence on the board

Songtext kommentieren

Log dich ein um einen Eintrag zu schreiben.
Schreibe den ersten Kommentar!

Ähnliche Artists

Quiz
Welcher Song ist nicht von Robbie Williams?

Fans

»Yampeza« gefällt bisher niemandem.