Ululu Songtext
von Eli Njuchi
Ululu Songtext
Ululu, ululu
Ululu, ululu
Ululu, ululu
Mmmh memories tend to ululu
When i remember we, mamie ululu
Angella wherever you are
Unayiwala kutenga ululu
Nzoveka unatenga zonse pochoka
Koma unayiwala kutenga ululu
Nzoveka ana onse unatenga
Koma unayiwala mmh
Ululu, ululu
Ululu kuwawa ululu
Ululu, ululu
Ululu, ululu
Ululu ah yeah ululu
Ululu kuwawa ululu
Ululu ah yeah ululu
Ululu, ululu
Kungonyamuka
No chifukwa
Mafunso kuchuluka
Misonzi
Pachiyambi zinali ngati ndiwo
Ka fungo chikoka pamphuno
Mtima wanga unati lero ndidya bwino
Chisoni, you used to say you love me
Promised to my heart you′ll never leave me
Now look what your lies have turned to, ululu
You used to say you love me
Promised to my heart you'll never leave me
Now look what your lies have turned to, ululu
Ah yeah ululu
Baby ululu
Ululu ah ululu
Ah yeah aah ululu
Ah yeah ululu
Ah yeah ululu
Njuchi ululu
Promised my heart you′ll never leave me (ululu)
Ululu, baby ululu
Kuwawa ululu (baby)
Ah yeah ululu
Ululu, baby ululu
Kuwawa ululu (baby!)
Ululu, ululu (the broken promises)
Ululu, kuwawa ululu
My heart is on fire (ululu)
Baby ululu
Ululu, kuwawa ululu
Nzoveka watenga zonse pochoka
Koma unayiwala kutenga ululu
Nzoveka katundu yense udatenga
Koma unayiwala kutenga ululu
Nzoveka mbale zonse udatenga
Koma udayiwala iwe kutenga ululu
Nzoveka anawo unatenga
Koma unayiwala (kutenga ululu)
Ululu, ululu
Ululu, ululu
Mmmh memories tend to ululu
When i remember we, mamie ululu
Angella wherever you are
Unayiwala kutenga ululu
Nzoveka unatenga zonse pochoka
Koma unayiwala kutenga ululu
Nzoveka ana onse unatenga
Koma unayiwala mmh
Ululu, ululu
Ululu kuwawa ululu
Ululu, ululu
Ululu, ululu
Ululu ah yeah ululu
Ululu kuwawa ululu
Ululu ah yeah ululu
Ululu, ululu
Kungonyamuka
No chifukwa
Mafunso kuchuluka
Misonzi
Pachiyambi zinali ngati ndiwo
Ka fungo chikoka pamphuno
Mtima wanga unati lero ndidya bwino
Chisoni, you used to say you love me
Promised to my heart you′ll never leave me
Now look what your lies have turned to, ululu
You used to say you love me
Promised to my heart you'll never leave me
Now look what your lies have turned to, ululu
Ah yeah ululu
Baby ululu
Ululu ah ululu
Ah yeah aah ululu
Ah yeah ululu
Ah yeah ululu
Njuchi ululu
Promised my heart you′ll never leave me (ululu)
Ululu, baby ululu
Kuwawa ululu (baby)
Ah yeah ululu
Ululu, baby ululu
Kuwawa ululu (baby!)
Ululu, ululu (the broken promises)
Ululu, kuwawa ululu
My heart is on fire (ululu)
Baby ululu
Ululu, kuwawa ululu
Nzoveka watenga zonse pochoka
Koma unayiwala kutenga ululu
Nzoveka katundu yense udatenga
Koma unayiwala kutenga ululu
Nzoveka mbale zonse udatenga
Koma udayiwala iwe kutenga ululu
Nzoveka anawo unatenga
Koma unayiwala (kutenga ululu)
Lyrics powered by www.musixmatch.com

