Songtexte.com Drucklogo

Too Long Songtext
von Eli Njuchi

Too Long Songtext

Sispense on the board
Eli

Too long
Mwina munandidumpha ndili pano
Pano, ay yah (ay yah)
Njuchi
Ndili pompaja pomwe munandisiya
Ndimkati mwina mudzanditenga
Kapena Galeta inandisempha
Nditume ngelo adzasiye uthenga
Sindinayambe lero
Ndalimbika limbika limbika
Ngati sindikumveka hello
Tadikira dikira dikira


Too long
Mwina munandidumpha ndili pano (it′s been too long)
Too long
Mwina munandidumpha been too long
Ay yah been too long
Ndili pompaja ponwe munandisiya
Ndimkati mwina mudzanditenga
Mu misonzi yanga ndikuyandamira
Mukachedwa mupeza ndamira
Kholo munalitenga
Katundu pakhomo anadzatenga
Omwe ndimati ndi azibale anga
Ndi amene akundisiya mulengalenga

Too long
Ndatopa nazo ndikufuna mpumulo
Zili ngati ndili mtulo
Ndikungofuna mundiuze dzuka anali maloto (yeah yeah yeah)

Pali njira zothetsela zonse
Tell me why sizitheka ndikati ndiziyese?
Mu dzenje la mikango mundipulumutse
Zikutenga nthawi kuti chingwe chindipeze
Ndine olephera pamaso pawo
Pa anthu onsewa zinagwera ine
Ndadikira dikira mdalitso


Tell me why now
Tell me God it's been too long
Mwina munandidumpha ndili pano
It′s been too long
Too long
Mwina munandidumpha been too long
Taking too long
Too long (too long)
Mwina munandidumpha ndili pano
It's been too long

Too long (too long)
Mwina munandidumpha been too long
Taking too long

Songtext kommentieren

Log dich ein um einen Eintrag zu schreiben.
Schreibe den ersten Kommentar!

Ähnliche Artists

Quiz
Welcher Song kommt von Passenger?

Fans

»Too Long« gefällt bisher niemandem.